Search the WhatsAd Community Intelligence index of WhatsApp groups to find the best ones.
1 result in the WhatsAd group index
ð®ð©ð®ð©ð®ð©ð®ð©ð®ð©ð®ð©ð®ð©ð®ð©ð®ð©ð¿ð¿ð¿ð¿ð¿ð¿ð¿ð¿ð¿ðŠð¹ðŠð¹ðŠð¹ðŠð¹ðŠð¹ðŠð¹ðŠð¹ðŠð¹ðŠð¹ð¥ð¥ð¥ð¥ð¥ð¥ð¥ð¥ð¥ðïžðïžðïžðïžðïžðïžðïžðïžðïž TAKULANDIRANI PANO PA F C B NYASA BG BULLETS GROUP ð¿ NTHAWI IKAKWANA ðððð¥ 10:30 PM GROUP LINO LIDZITSEKEDWA POFUNA KUTETEZA GROUP LINO KWA ANTHU OMWE AMAKONDA KUTUMIZA ZITHU ZOSAKHARA BWINO ANTHU AKAGONA M'MA GROUP NDIPO LIDZITSEKULIDWAððð¥ 5:30AM NDIPO MARAMURO ALI MOTERE ð ð ð ð ð SUNDAY LILILONSE MUZIYENDA CHIKOLOPA MUNO KUSABURA AMENE SAKUTENGA NAWO GAWO MUNO 𫵠𫵠𫵠𫵠𫵠𫵠𫵠𫵠𫵠DZIWANI KUTI UKAPEZEKA PANO UKUYENERA KUMATENGA NAWO GAWO PA NKHANI ZAMASEWERO KOMASO MACHEZA FOLLOW ðððððð¥ RAMULO (1). OSATUMIZA MA BUSINESS KAPENA ZA USING'ANGA MUNO â RAMULO (2). OSATUMIZA MA LINK AMA GROUP ENA MUNO â RAMULO (3). OSATUKWANA MUNO âKAPENA KUNYOZERANA ZIPEMBEDZO â RAMULO (4). OSATUMIZA NKHANI ZOPANDA UMBONI MUNO â RAMULO (5). OSARANKHURA VN MUNO NGATI USANAPEPHE CHILOLEZO KWA ADMIN â SUNDAY LILILONSE MUZIYENDA CHIKOLOPA MUNO KUSABURA AMENE SAKUTENGA NAWO GAWO 𫵠𫵠𫵠𫵠𫵠RAMULO (6). OSAIMBA GROUP CALL MUNO â RAMULO (7). NDI UFULU WANU KUTUMIZA NKHANI ZAMASEWERO â KUCHOKERA PA WAIRES ZOSIYANA SIYANA ANGAKHARESO MA CHANNEL OSIYANA SIYANAâ RAMULO (8). OSATUMIZA MA VIDEO ORAULA KOMASO MA PHOTO MUNO â TENGANI GAWO PA NKHANI ZAMASEWERO NGAT ULI SAPOTA WENI WENI WA BULLETS ð®ð© TIYENI TITSATILE MARAMURO POFUNA KULIMBIKITSA UMODZI, CHIKONDI, NDI CHIKOKA CHA GROUP LINO TIMAKUNYADIRANI MAPARE STNA ANZATHU ð®ð©ð®ð©ð®ð©ð®ð©ð®ð©ð®ð©ð®ð©ð®ð©ð®ð©ðŠð¹ðŠð¹ðŠð¹ðŠð¹ðŠð¹ðŠð¹ðŠð¹ðŠð¹ðŠð¹ð¿ð¿ð¿ð¿ð¿ð¿ð¿ð¿ð¿ð¥ð¥ð¥ð¥ð¥ð¥ð¥ð¥ð¥ ðïž ðïž ðïž ðïž ðïž ðïž ðïž ðïž âœ âœ âœ âœ âœ âœ âœ âœ ðïžðïžðïžðïžðïžðïžðïžðïžðïž
Verified invite link, member details and advertising options on WhatsAd.
*MALAMULO ATHU MUNO MU BULLETS MANOMA SILVER ð¥ ZAMASEWERO* âœâœâœ (1) alendo khalani omasuka potenga nawo mbali mu zochitika za group lino (2) *timakamba nkhani zokhuza mpira 95% zakunja kwa mpira 5%* (3) 99% zilankhulo zovomerezeka chichewa English 1% zilankhulo zina (4) *sitimalola kupanga recode kuponya ma link ama group ena ndi ma sticks ena ali onse muno* (5) matsiku ena timakhala ndi ma program monga Monday timakhala ndi mulendo wathu Friday top 20 munthawiyi sitimalola munthu kuponyapo nkhani zakunja kwa program yo mukagotero remove pompo pompo (6) *kusalana kapena kusankhana pa group chifukwa chosiyana zipembezo kapenanso mitundu nkolesedwa* (7) member yemwe sanalowe nawo mu top 20 kwa 2weeks kapena osakwanisako 30 messages adzachotsedwa (8) *tiyeni tipasane ndi kusungilana ulemu polankhula komanso pano sipopezera mkazi / mamuna chonde guys anthufe ndife akulu akulu komanso ndife pachibale za pa group zizithera pa group pompano* (9) group lino sitimalola kubweresa ma update onama pano ukangopezeka pompo pompo remove (10) *ma dmin athu nawonso ndi anthu ali ndi kufooka kwawo ngati alankhula china chake chosakhala bwino ndi ufulu wa member wina aliyense kuzuzura mwaulemu osati monyoza ayi* (11) ma dmin athu samatulutsa munthu mopanda chifukwa ziwani kuti mukangotulutsidwa simuzapangidwanso add ndiye chonde osamabwera ku in box kwa admin *mukangosunga zomwe mwauzidwa panozi ziwani kuti mukhalitsa muno mpaka kale* mphavu nyerere ðððððð³ðð³ðð³ðð³ mphavu bullets ðŠð¹ðŠð¹ðŠð¹ðŠð¹ mphave silver ðŠð·ðŠð·ðŠð·ðŠð· *umodzi pa machedza* ð€žââð€žââð€žââð€žââð€žââ
1ïžâ£Osasitha chithuzi kapena mutu wa gulu 2â£Ma videos olaula muno ayi or pic. 3ïžâ£Osatumiza link ya group lina muno ayinso 4ïžâ£No voice messages /stickers ð¯. 5ïžâ£Muno simosewela koma kugawana Sports ndi Tinkhani patali patali 6ïžâ£kumatengapo mbali osamangoti duu muzatulusidwa. 7ïžâ£Ulemu kwa aliyese. 8ïžâ£Nkhan zaku inbox zithere Komweko. 9ïžâ£Ngati member wa group waona povuta pena pake pita kwa admin aliyese muuze kuti akuthandize ð Kusarana ziyankhulo muno ai or zipembezo tose ndife amodzi amalawi. 11. Aziwitseni anthu zomwe mwatumiza kupanda kutero mupedzeka panja ð *By Admin*
Malamulo aa group ali mothelo 1 Vn yoletsedwa ââ 2 macheza katiti â â 3 Voice chat yoletsedwa ââ 4 kutukwanana muno ay ââ 5 Nkhani za mpira â â â 6 ma stick No ââ 7 mautenga okuza team ina ay ââ 8 ma link aa group lina ay â â 9 Lamulo lomaliza chonde mokumbepa all members monga masapoter aa team yathu ya NBB NYASA BIG BULLETS chonde osanyosa ma admin tikale okondana kulakwisa admin timausana kut tikotse mvuto limenelo zikomo maule notse ððððð
1 Osasitha chithunzi kapena mutu wa gulu ââââ 2 Ma videos olaula or pic muno ayiii..ð«ð«ð«ð«ââââ 3 Osatumiza link ya group lina muno âââââ 4 No voice messages/ stickers.ââââ 5 Muno simosewela komo kugawana NKhani ndi Sports.â 6 Kumatengapo mbali osamangoti duu muzatulusidwa.â 7 Ulemu kwa aliyese ndiofunikaâ 8 Nkhani zaku inbox zithere Komweko Osazibweretsa Panoâ 9 Ngati member wa group waona polakwika alowe ku inbox kwa admin Kuti Amthandizeâ 10 Kusarana ziyankhulo muno ai or zipembezo tose ndife amodzi amalawi.ð«ð«ð«ââââââ 11 Aziwitseni anthu zomwe mwatumiza kupanda kutero mupedzeka panja.â ð by Admin
ððððð ððð ððððððð ð¬ð¶ð ð«ð ðð£ðšð«ðšð£ð¶ð ððžððžðððð ðžððððððŒð KUPEZEKA UTAPONYA LINK YOSIYANA NDI GROUP INO REMOVE ââ KUNOKO NDIKWA MAULE NSITUKUFUNA NEBA UKAPEZEKA REMOVE ââ KUPONYA DZOLAULA UKANGOPEZEKA REMOVE ââ VN OR VOICE CHAT ð STICKERS NSITIMAGWILISA NTCHITO CHIFUKWA KUPEZE KWA BUNDLE NDKOSIYANAââ KUCHEZA MOSASAKHANA MITUNDU KOMASO KOCHOKELA POTI TOSE NDIFEANA ABANJA LIMOZIð¥ð¥ð¥ð¥ð¥ ALIYESE ALINDIKUTHEKELA KOPONYA KHANI OR VIDEO KOM ZOKHUZA BULLETS OSAPONYA ZOSIYANA UKANGOTELE REMOVE ââ KWAMEN AKUZIWA KUTI CHILIPO CHOLAKWIKA KOM MULIOMASUKA KUWAPEZA ADMIN NDIKUWAFOTOKOZELA KUTI MUZIYENDELABE LIMOZI GROUP THAWI IKAKWANA 09:30PM TIZILISEKA KUPANGILA AKAPASULE KUONONGA ASING'ANGA PEZANI GROUP YANU ððð§°âïžâïž ððððððððâ€ïžâð¥â€ïžâð¥â€ïžâð¥ MAULEð¥ð¥ð¥ MOTO TINABWELA KUZAKHALAâœâœâœâœâ â â ð€ð€ð€
MWALANDILIDWA NONSE NDIPO KHALANI OMASUKA. ALENDO MUKANGOLOWA KUMENE PONYANI PIC NDIPO MUDZIFOTOKONZERE NOKHA KUTI NDINU NDANI NDIPO MUMAKHALA KUTI. NDIPO TSATILANI MALAMULO ONSE AMGULU LINO MUKATERO MUDZAKHALITSA. LEMEKEZANI MALAMULO AMGULU LINO NDIPO NAWO ADZAKULEMEKEZANI. GROUP CREATED BY ABDUL RASHID CHIKOPA.