Search the WhatsAd Community Intelligence index of WhatsApp groups to find the best ones.
1 result in the WhatsAd group index
Malamulo a Muno ------------------------------ (1)Kupempha ndikutumiza nyimbo. (2)Nyimbo zake ziyambire 2010 kumatsika kumusi. (3)Osatukwanana wina ndimzake timalimbikitsa ubale muno. (4) Osatumiza link or ma Photo olaura kapenanso zosemphana ndi group lino muzachotsedwa. (5)Osanyozerana mtundu kapena chipembedzo tonse ndi amodzi. Komaso osaponya ma sticker muno ayi (6)Ndi udindo wa aliyense kutumiza ndikupempha nyimbo zakale koma ngati mwafuna zatsopano pemphani ku inbox ena azakupatsani komweko. (7) Ma voice note siololedwa muno koma zikavutitsitsa kuti mufuna nyimbo nde mutu wake simukuudziwa funsani admin aliyense kuti mumumvetseletse Voice note ndipo akusakireni . (8)Osatukwana muno tili ndi anthu akulu akulu azaka zapakanthawi omwe amafunika kuwalemekeza. Tiyeni titsate malamuro kuti tipitilize kusangalara ndinyimbo komanso zochitika zotikumbutsa kale lathu .
Verified invite link, member details and advertising options on WhatsAd.
*NYIMBO ZOTAMANDA KOMANSO KUKWEZA YEHOVA*
‼️‼️Market place 🔨📞🚙💿🖥️📲📱🗜️⌚📸📷‼️‼️ 1️⃣Buying and selling 2️⃣ cape town people chete 3️⃣ No violence 4️⃣ Language shona 5️⃣ Price💰 and location 🏘️ 6️⃣Respect is very important 7️⃣ No links ❌❌❌🚮🚮 💚💚 👏👏 thank you🩵🩷❤️🧡💛💚🇿🇦🇿🇦[link hidden — subscribe to view]?mode=hq2tswa
Kaleem Trusted Services 🚀* *Group Guidelines 📝* Hello everyone! I'm Rai Kaleem 🙋♂️. 😉 Let's keep our group respectful and safe 🤝. *Rules:* 1️⃣ Respect each other 🙏 2️⃣ Deals through admin only 🤝 3️⃣ No scams allowed 🚫 *Why deal through admin? 🤔* - Safe and secure transactions 🔒 - Admin guarantee protects you 🛡️ - Avoid scams and issues 🚫 * _*Disclaimer 🚫*_ * *links not allowed* *Let's work together! 🌟* Join us and follow the rules for a positive experience 😊. Best, Kaleem Ullah *Join Our Group 🤝* [link hidden — subscribe to view]?mode=ems_copy_t *Thanks for reading! 😊*
*WELCOME TO KUGAWANA NYIMBO MWAKATHITHI*. 🫂🎧🎧🎼🎵🎵🎶 *MALAMULO ATHU ALIMOTELE👇🏼👇🏼*. *1.🛑ukangojoina kumene group yambakaye waponya pic... Yako ndikuzilongotsola dzina lako ndikomwe ukuchokera*. *2.🛑Tilemekedzane wina ndinzache posatengera mtundu kapena chipembedzo or kochokera*.❌❌⛔📛🚫 *3.🛑No ma videos kapena zithunzi zolawula muno even ma voice notes❌❌⛔📛🚫ukangopedzeka remove🎬🚮*. *4.🛑No any foreigner groups/links, ma short videos or stickers muno ayi❌❌⛔📛🚫ukangotumidza basi uwona nsana wanjira🎬🚮*. *5.🛑ndiudindo wawina aliyense otumidza nyimbo muno osamangodikira ma admin okha kuti atumidze nyimbo❌❌⛔📛🚫*. *6. 🛑Then usanapemphe nyimbo yamba kaye waponya nyimbo zomwe iwe ulinazo ndipo ife tizakuthandidza the same time*. *7.🛑Kupempha mowirikidza koma iwe osatumidza zimenezo ayinso❌❌⛔📛🚫ma camera akakuwona 👀basi remove ndiyomweyo🎬🚮*. *8.🛑Ndipo osatenga nawo gawo pa maprograms amenewa timasazikana naye mosayang'ana nkhope🤣❌❌⛔📛🎬🚮*. *⚠️🚸WARNING: ngati wapedza kt group lakiyidwa🔐🔐🔒🔒osafunsa kt why?❌❌⛔📛 Udzalandira remove 🎬🚮ndekuti ma admin akukonza zina zake zosemphana ndi group*. *#. ✅✅Tsatilani zimenezi kt matsiku anu okhala muno achuluke musanawone nsana wanjira ngati omwe adawona John chilembwe kumandala😉*. *#. ✅✅Machedza wez koma nyimbo kathithi...*. *WROTE BY ALL ADMINISTRATOR OFFICCERS, MWAKOMA NONSE🥳🥳💃🏻💃🏻🤼♀️🤸🏻♀️🤸🏻🏋🏻♀️🙊🙌🏻🙌🏻*.
TAKULANDIRANI KUNO KUCHIMAKE KWA NYIMBO KANTHITHI MARAMURO ALI MOTERE👇👇 (1). Osatumiza link ya group Lina muno (2). Muno ma voice recording ayi aliyense akuyenera kulemba basi (3) kutumiza ma vedio kapena zithunzi zolawura muno ayi (4) Ukaponya nyimbo kapena vedio ukuyenera kulemba title ndamene anayimba (5) kulemba title zimathandiza munthu kut usatenge nyimbo yomwe uli nayo kale (6) Zosakhana mitundu muno ayi tonse ndife amodzi, nkhani za mipingo, ndale ndi mpira muno ayi BY ADMIN ✍️✍️✍️✍️✍️. .......
Admin amakhala Lilongwe kaphiri area 38 Muno sitiba team up bas