Search the WhatsAd Community Intelligence index of WhatsApp groups to find the best ones.
1 result in the WhatsAd group index
*JOIN NOW* *π―% secure and genuine* *No scamsβ* *100% Real and Legitπ―*πππππππππ *[link hidden β subscribe to view]* *[link hidden β subscribe to view]* *[link hidden β subscribe to view]* ππππ *ππΎThis platform is 100% real and legit with a large number of users earning daily from it. You should be a part of this platform and start earning from it daily...*
Verified invite link, member details and advertising options on WhatsAd.
*MALAMULO ATHU MUNO MU BULLETS MANOMA SILVER π₯ ZAMASEWERO* β½β½β½ (1) alendo khalani omasuka potenga nawo mbali mu zochitika za group lino (2) *timakamba nkhani zokhuza mpira 95% zakunja kwa mpira 5%* (3) 99% zilankhulo zovomerezeka chichewa English 1% zilankhulo zina (4) *sitimalola kupanga recode kuponya ma link ama group ena ndi ma sticks ena ali onse muno* (5) matsiku ena timakhala ndi ma program monga Monday timakhala ndi mulendo wathu Friday top 20 munthawiyi sitimalola munthu kuponyapo nkhani zakunja kwa program yo mukagotero remove pompo pompo (6) *kusalana kapena kusankhana pa group chifukwa chosiyana zipembezo kapenanso mitundu nkolesedwa* (7) member yemwe sanalowe nawo mu top 20 kwa 2weeks kapena osakwanisako 30 messages adzachotsedwa (8) *tiyeni tipasane ndi kusungilana ulemu polankhula komanso pano sipopezera mkazi / mamuna chonde guys anthufe ndife akulu akulu komanso ndife pachibale za pa group zizithera pa group pompano* (9) group lino sitimalola kubweresa ma update onama pano ukangopezeka pompo pompo remove (10) *ma dmin athu nawonso ndi anthu ali ndi kufooka kwawo ngati alankhula china chake chosakhala bwino ndi ufulu wa member wina aliyense kuzuzura mwaulemu osati monyoza ayi* (11) ma dmin athu samatulutsa munthu mopanda chifukwa ziwani kuti mukangotulutsidwa simuzapangidwanso add ndiye chonde osamabwera ku in box kwa admin *mukangosunga zomwe mwauzidwa panozi ziwani kuti mukhalitsa muno mpaka kale* mphavu nyerere ππππππ³ππ³ππ³ππ³ mphavu bullets π¦πΉπ¦πΉπ¦πΉπ¦πΉ mphave silver π¦π·π¦π·π¦π·π¦π· *umodzi pa machedza* π€Έββπ€Έββπ€Έββπ€Έββπ€Έββ
Malamulo aa group ali mothelo 1 Vn yoletsedwa ββ 2 macheza katiti β β 3 Voice chat yoletsedwa ββ 4 kutukwanana muno ay ββ 5 Nkhani za mpira β β β 6 ma stick No ββ 7 mautenga okuza team ina ay ββ 8 ma link aa group lina ay β β 9 Lamulo lomaliza chonde mokumbepa all members monga masapoter aa team yathu ya NBB NYASA BIG BULLETS chonde osanyosa ma admin tikale okondana kulakwisa admin timausana kut tikotse mvuto limenelo zikomo maule notse πππππ
1 Osasitha chithunzi kapena mutu wa gulu ββββ 2 Ma videos olaula or pic muno ayiii..π«π«π«π«ββββ 3 Osatumiza link ya group lina muno βββββ 4 No voice messages/ stickers.ββββ 5 Muno simosewela komo kugawana NKhani ndi Sports.β 6 Kumatengapo mbali osamangoti duu muzatulusidwa.β 7 Ulemu kwa aliyese ndiofunikaβ 8 Nkhani zaku inbox zithere Komweko Osazibweretsa Panoβ 9 Ngati member wa group waona polakwika alowe ku inbox kwa admin Kuti Amthandizeβ 10 Kusarana ziyankhulo muno ai or zipembezo tose ndife amodzi amalawi.π«π«π«ββββββ 11 Aziwitseni anthu zomwe mwatumiza kupanda kutero mupedzeka panja.β π by Admin
πππππ πππ πππππππ π¬πΆπ π«π ππ£π¨π«π¨π£πΆπ ππΈππΈππππ πΈππππππΌπ KUPEZEKA UTAPONYA LINK YOSIYANA NDI GROUP INO REMOVE ββ KUNOKO NDIKWA MAULE NSITUKUFUNA NEBA UKAPEZEKA REMOVE ββ KUPONYA DZOLAULA UKANGOPEZEKA REMOVE ββ VN OR VOICE CHAT π STICKERS NSITIMAGWILISA NTCHITO CHIFUKWA KUPEZE KWA BUNDLE NDKOSIYANAββ KUCHEZA MOSASAKHANA MITUNDU KOMASO KOCHOKELA POTI TOSE NDIFEANA ABANJA LIMOZIπ₯π₯π₯π₯π₯ ALIYESE ALINDIKUTHEKELA KOPONYA KHANI OR VIDEO KOM ZOKHUZA BULLETS OSAPONYA ZOSIYANA UKANGOTELE REMOVE ββ KWAMEN AKUZIWA KUTI CHILIPO CHOLAKWIKA KOM MULIOMASUKA KUWAPEZA ADMIN NDIKUWAFOTOKOZELA KUTI MUZIYENDELABE LIMOZI GROUP THAWI IKAKWANA 09:30PM TIZILISEKA KUPANGILA AKAPASULE KUONONGA ASING'ANGA PEZANI GROUP YANU πππ§°βοΈβοΈ ππππππππβ€οΈβπ₯β€οΈβπ₯β€οΈβπ₯ MAULEπ₯π₯π₯ MOTO TINABWELA KUZAKHALAβ½β½β½β½β β β π€π€π€
MWALANDILIDWA NONSE NDIPO KHALANI OMASUKA. ALENDO MUKANGOLOWA KUMENE PONYANI PIC NDIPO MUDZIFOTOKONZERE NOKHA KUTI NDINU NDANI NDIPO MUMAKHALA KUTI. NDIPO TSATILANI MALAMULO ONSE AMGULU LINO MUKATERO MUDZAKHALITSA. LEMEKEZANI MALAMULO AMGULU LINO NDIPO NAWO ADZAKULEMEKEZANI. GROUP CREATED BY ABDUL RASHID CHIKOPA.
MALAMULO A GROUP LINO NDI AWA CHONDE YESETSANI KUTSATILA MALAMULOWA NDIKUTI TIKHALILE LIMODZI UMUTU MULI KHANI ZA MPILA ZOKHA ZOKHAπ―π―π―π―π― β¬οΈβ¬οΈβ¬οΈ (1)SITIMALOLA MA (VN) (2) OSATUMIZA LINK ILIYONSE (3)OSAPONYA STICKER ILIYONSE (4)OSATUMIZA MA VIDEO OLAULA (5)OSATUKWANANA KAPENA KUNYOZANA IZI NDI ZA MPILA (6)ONESETSANI KUTI KHANI MWATUMIZAZO NDI ZOONA (7)TENGANI NAWO GAWO POTUMIZA KHANI ZA MPILA ZIMENE ZAKUPEZANI KUPANDA OSATELO KWA MWEZI MUZACHOTSEDWA (8)KHANI ZA PA WAILESI ZIMENE ZAULUTSIDWA KUMENE MUKHOZA KUPONYA TIDZAKHALA OKONDWA KWAMBIRI NGATI MUTATSATILA MALAMULOWAπ€π€π₯π₯π₯π₯π₯³π₯³π₯³β½β½β½β½