Search the WhatsAd Community Intelligence index of WhatsApp groups to find the best ones.
1 result in the WhatsAd group index
Welcome pa mrakatuli wapamphata;;;; chonde satilani izi kuti mukhalitse👇👇. 1, ngati mwalowa kumene khalani odekha chifukwa mutha kutulusidwa popopo, 2, mono zoponya zolaula ayi ukapezeka ulongeza kusadache, 3,cholinga cha group lino ndikupasana ndakatulo,komanso macheza,, 4,sitilola munthu kulo ku inbox Kwa mnzake opanda kupempha ukapezeka out. 5,ngati mwapeza vuto mu group ili aziwiseni addim ndipo akuthandizani. 6,anthu timapanga add loweluka lokha basi komanso ili nditsiku limenenso timabweresa chikolopa chosetsa onse ongofuna kuzadzitsa pa group pano 7,ngati mwakonda munthu mupempheni popa before kumulowera Ku inbox .. 8 loweluka lililonse tizikhala ndi pic day pachifukwa ichi aliyense akupemphedwa kutenga nawo gawo osateroyo out
*PLEASE ATTETION* 🙏🙏 *Muli bwanj kose Muli mwalandridwa group lino nkhan Nd kugawana malink bas nyimbo,nkhan,chilichose Muno Nd choloredwa kupatula kutukwana Nd zo laula bas* *Nd ma recorder* *Machezaso Muno Nd ororedwa km Chichewa Nd chingerez KT tizane bas* *TIVELANE KM CHINTHU ICH PLZ OSAPONYA KAMBILIMBLI LINK IMOZMOZ KUPONYA KAMOZ ANTHU NGAT AIKONDA ALOWA BAS UKAPEZEKA ROMOVE ZBWANA TIMAKANA MUMUNO*💪 *Mmalo mwa madmn ose Nd ngot MWAKOMA nose*🙏🙏🙏🙏🙏👇👇👇👇🤸🤸
Tigawane ma link""";;; udindo otumiza link muno ndi wa wina aliyense, pemphani ndipo muzapasidwa, ndipo nkhani yathu muno ndi ma link bas zinazo osaponya muno usanafunse uzachitidwa remove, macheza abwino zikomo.
Verified invite link, member details and advertising options on WhatsAd.
*TAKULANDILANI* *KUNO SITIPONYAKO MA FLIM MWAKATHITHI* *KUNO NIMANGOKUDZIWITSANI ZA MA FLIM OMWE ATULUKA KAPENA OMWE ATULUKE* *NGATI MUKUFUNA MUZIPEZA MA FLIM OSE MWADONGOSOLO MUKUYENELA KULIPILA KUTI NIKUPANGENI ADD PA GROUP MBAMBANDE YACHANGU NI YODALILIKA* 0994167642 or 088427789 kmso 0995580610