Search the WhatsAd Community Intelligence index of WhatsApp groups to find the best ones.
1 result in the WhatsAd group index
TAKULANDILAN ALENDO MUNO PEZANI WACHIKNDl WANU Lemekezani malamulo ๐๐ 1 Ukalowa ponya PIC ndikomwe umakhala 2 Ukafuna kucheza ndimkazi ku inbox uza ky admin 3 Osaponya ma Link a group yina โ 4 Audio or VN Ayi 5 muno ukapezeka ukulemba English โ 6 Ndiufulu waliyese kuponya mapono 7 Ngat sukutengapo mbali pa nkhani zose โ 8 Ngat ndi Stick yapono utha kuponya 9 Tsiku laTopic ndi limodz lachiwir madzulo kuyamba 7 o'clock 10 Tikhale okondana kuti group la2 lipite patsogolo 11 Oyambitsa voice chat join limove โ Lemekezan malamulo kuti masiku amuno achuluke
Verified invite link, member details and advertising options on WhatsAd.
MALAMULO:::::::::::::::::::::::::::::::::: (1) WOSAPONYA LINK YA GROUP LINA (2) ZANDALE KAPENA ZACHIPEMPHEZO NDI KUNYOZANA MUNO AYI ZIMENEZO AWA NDIMACHEZA TIYENI TIKONDANE WINA NDIZAKE (3) WOSATUMIZA CHINTHU CHOKHUZA ZOLAULA MUNO (4) WOSAYIMBA VOICE CALL PA GROUP (5) NGATI MUKUCHEZA NDI ZANU PANKHANI ZA MPIRA CHEZANI BWINOBWINO POSADUMPHA MALILE A ULEMU (6) SUNDAY TIMAKHALA NDI PIC DAY NDICHOLINGA CHOTI TIZIWANE (7) ZIWANI KUTI NDIUDINDO WAWINA ALIYESE KUTUMIZA ZINTHU ZOKHUZA MASEWELO A MPIRA KUTI GROUPLI LIBHEBHE ZIKOMO MAKOMA NONSE MASAPOTA A MA TEAM WOSIYANASIYANAโ๏ธ
WELENGANI MUSANAPANGE JOIN PLEASE : NTCHITO YA ADIMIN๐ฅ๐ฅ๐ฅ๐ฅ๐๐๐ CHOLINGA CHA GULU LINO KUDZIWITSA MOMWE AKUTULUKILA MA FLIM A CHICHEWA KWA ONSE AMAWAFUNA. TIMADZIWITSA POTUMIZA KWA MA CUSTOMER ATHU IZI 1..Entertainment ๐ฅ๐ฅ 2..part imodzi ya filim๐ฅ๐ฅ 3..Poster ya filim๐ฅ๐ฅ 4..Nthawi yomwe yatuluka filim timapanga screenshot ๐ฅ๐ฅ 5..Nthawi yomwe tatumizila pa VIP timapanga screenshot ๐ฅ๐ฅ DZIWANI KUT MUKALIPILA KAMODZI MUZILANDILA MA FILIM PA V.I.P๐ฅ๐ฅ TSIKU LILILONSE PA WEEK KOMANSO PA MWEZI MOSAVUTA MUNTHAWI YAKE YOMWE YATULUKILA FILIM. Talk TO ME INBOX CHAT WHILE I'M ONLINE๐ฅ๐ฅ. NDIYANKHULEN KU INBOX NDILI ONLINE๐ฅ๐ฅ. ZIKOMO. [link hidden โ subscribe to view]