Search the WhatsAd Community Intelligence index of WhatsApp groups to find the best ones.
1 result in the WhatsAd group index
Verified invite link, member details and advertising options on WhatsAd.
*MALAMULO ATHU MUNO MU BULLETS MANOMA SILVER ð¥ ZAMASEWERO* âœâœâœ (1) alendo khalani omasuka potenga nawo mbali mu zochitika za group lino (2) *timakamba nkhani zokhuza mpira 95% zakunja kwa mpira 5%* (3) 99% zilankhulo zovomerezeka chichewa English 1% zilankhulo zina (4) *sitimalola kupanga recode kuponya ma link ama group ena ndi ma sticks ena ali onse muno* (5) matsiku ena timakhala ndi ma program monga Monday timakhala ndi mulendo wathu Friday top 20 munthawiyi sitimalola munthu kuponyapo nkhani zakunja kwa program yo mukagotero remove pompo pompo (6) *kusalana kapena kusankhana pa group chifukwa chosiyana zipembezo kapenanso mitundu nkolesedwa* (7) member yemwe sanalowe nawo mu top 20 kwa 2weeks kapena osakwanisako 30 messages adzachotsedwa (8) *tiyeni tipasane ndi kusungilana ulemu polankhula komanso pano sipopezera mkazi / mamuna chonde guys anthufe ndife akulu akulu komanso ndife pachibale za pa group zizithera pa group pompano* (9) group lino sitimalola kubweresa ma update onama pano ukangopezeka pompo pompo remove (10) *ma dmin athu nawonso ndi anthu ali ndi kufooka kwawo ngati alankhula china chake chosakhala bwino ndi ufulu wa member wina aliyense kuzuzura mwaulemu osati monyoza ayi* (11) ma dmin athu samatulutsa munthu mopanda chifukwa ziwani kuti mukangotulutsidwa simuzapangidwanso add ndiye chonde osamabwera ku in box kwa admin *mukangosunga zomwe mwauzidwa panozi ziwani kuti mukhalitsa muno mpaka kale* mphavu nyerere ðððððð³ðð³ðð³ðð³ mphavu bullets ðŠð¹ðŠð¹ðŠð¹ðŠð¹ mphave silver ðŠð·ðŠð·ðŠð·ðŠð· *umodzi pa machedza* ð€žââð€žââð€žââð€žââð€žââ
ENTRE NOUS HOMMES.... Ici on propose des solutions pour : ð ðððððððŠðŠððŠ ðŠÂ£ð«ðšðððð (érection, énergie, confiance) ð ððð¥ðð¡ðððŠðŠðð ðð¡ð§ ðð ð£Ãð¡ððŠ (ð²ð ðð¹ð¹ðŒð»ðŽð²ð¿) ð ðŠðð¡ð§Ã ð©ðð¥ððð (ððŒð¿ð°ð² ð¶ð»ðéð¿ð¶ð²ðð¿ð², ðð¶ð² ð±âðµðŒðºðºð²) ð¡ ðð²ð ððŒð¹ððð¶ðŒð»ð ðð¬ð¬% ð»ð®ððð¿ð²ð¹ð¹ð²ð, ð±ð²ð ð°ðŒð»ðð²ð¶ð¹ð ðœðð¶ððð®ð»ðð, ð±ð²ð éð°ðµð®ð»ðŽð²ð ðð¿ð®ð¶ð. ð§ð ð²ð ð®ð ð¯ðŒð» ð²ð»ð±ð¿ðŒð¶ð. ð¡ð² ðŸðð¶ððð² ðœð®ð ð°ð² ðŽð¿ðŒððœð². ðð² ðŸðð² ðð ðð®ð ð®ðœðœð¿ð²ð»ð±ð¿ð² ð¶ð°ð¶ ðœð²ðð ð°ðµð®ð»ðŽð²ð¿ ðð® ðð¶ð² ð±âðµðŒðºðºð². ðð¿ ððŒðð°ðŒ ðŠð²ð¿ðð¶ðð²ðð¿ ðŠðŒð°ð¶ð®ð¹ð©ºð¥Œ
Mutemo wetinao mugrup no kufonamugrupâstk eniweyi stk noâ Amusendiwi Pono né foto âamutukuwani wajoimua usingazvidi left wakanharara usatuka. Group romutambo wakabhudisua ndi DJ MAVUNDURE ðð€ð¹ðžð¥ð€NDHINDHA NOCHIZEPETE. tora Ngoma yamavundure uzwe ndhapi tapi dj mavundure MORAMBASWINA PRODUCTIONð¹ð¥ïžð±ïžðšïžð¥ð¥ wanessa pa MOZAMBIQUE ..cell number âðŒ[contact hidden] [contact hidden] [contact hidden] [contact hidden] M V-STUDIO. Whatsapp , you tube, Facebook REEFA!!! ð€ðïžððð²ð€ð€ 6:00ð10:00ð
Ringi âAidiwi âkutukana âno Mafarocheteâ no Mangomaâ no maponoâ no mavidiyo â okusekejanaâ ð©·â€ïžð©µððâ€ïžâð¥ð©¶ð€ððððððâïžððð§ð€ðžð¥ðªð¥ðððððð¥âªâ©â®ïžâ«â¬âïžðŒðµð¶ð¿ðŒð¿ðŠð²ð¿ð¢ð¢ð¢
NBBðŠð¹ðŠð¹NOMAðªðºðªðºSILVER STRIKERSð§ðŒð§ðŒ Takulandilan ku group la masapota ampira okonda ma team awo mwamtendere. Muno timalimbikisa kukondana wina ndi mzake osat mikangano koma macheza okhuza mpira bas. Ochilimika kuponya nkhan pazikhakala mwayi wa mphoto ya ma bundle a internet *Malamulo agroup lino* Zolesedwa 1.osaponya link la group Lina ââââukatero remove 2.osaponya chilichonse choonesa kulaulaââââukatero remove 3.osachula maina oyambisa mikangano muno monga:kapado/nkhumba fc,chingambwe fc,nyau fcââââ ukapezeka remove. 4.osaponya ma sticker,voice note,kutukwanaââââUkapezeka remove 5.siku la mpira(match day)ndi siku longoponya ma updade osasakaniza nkhan kupereka mpata kwa mamembala kusatira mpira. 6.kupereka update yabodzaââââ Ukapezeka remove 7.kusakhala active kwa 2weeksââââremove 8.Ili ndi group la za mpira only osatumiza zosemphana ndi mpira monga za ndale,nkhan osat zampiraââââukapezeka remove 9.ukalowa pa chat kukakhala game tiziyesesa kusatila mamessage omwe atizidwa kale kut tione mmene ma results mmene akuyendera kupewa mafunso ot game ikuyenda bwanji,wagolesa ndan,zikutha bwanji,izi zimapwetekesa omwe amuluza. 11.oyambisa chisokonezo munoââââremove *Kutumiza nkhan ndi kwa aliyense osadikilira ma admin okha* Ngat mwawona vuto pa malamulowa pezanani ndi admin ndipo tulani nkhawa zanu. Masiku ena tizikhala ndi mway ocheza ndi alendo koma a mpira okhaokha. *Maule,manoma ndi ma bankers ð©ð©ð©ðŠð¹ðŠð¹ð¬ð·ð¬ð·ð¬ð·ðªðºðªðºðªðºð§ðŒð§ðŒð§ðŒð§ðŒpamodz imapanga flamesð²ðŒ* Zikomo khalan omasuka *By adminstration*