Search the WhatsAd Community Intelligence index of WhatsApp groups to find the best ones.
1 result in the WhatsAd group index
Verified invite link, member details and advertising options on WhatsAd.
MUSATUMIZE LINK LA GROUP INA OSAPONYA ZOLAULA AI MUKAKONDA KATUNDU INBOX 📥 ME OR PA GROUP POMPA ZIMATHEKA KATUNDU TIMATUMIZA NGATI MLI KUTALI MALAWI KOMASO KWINA TRANSPORT IMAKHLA LA CUSTOMER. MONDAY TIMATUMIZA KATUNDU KU SOUTH AFRICA 🌍 WELCOME 🤗
WELCOME DEAR CUSTOMER MUNI NDIMA KHALA NDIKATUNDU WA AVAILABLE KULIPILA KUTENGA KUTALI NDIMATUMIZA THROUGH (SPEED,CTS,POST OFFICE AND BUSSES) NGAT MWAKONDA CHITHU NDIYAKHULEN IN BOX ZIKOMO
24 hrs online
*MALAMULO A GROUP INO ALI MOTELE* ~Alendo nonse mwalandilidwa group ino timagulitsa zovala mukakonda inbox apo ai pa group papa mutha kusakha zomwe mwafuna... Katundu timatumiza kulikonse ngati customer achikonda kma transport imakhala la customer. Mukuponya zosephana ndi group ino timapanga remove apo ai kutseka group. Mukalipira musaiwale screenshot ngati maumboni plus kundipasa ma details anu.. Katundu timatumiza use. 1. Post office 2. CTS 3. Bus ulemu 4. Speed Ena tili dziko la South Africa.. Timatumiza use Bus... Katundu omwe tidziponya muno. Wina Ali ready available Wina ai.. Order timapanga Monday up to Friday katundu afika Monday Ngati katundu wanu omwe mukumufunayo kulibe.. munthu amalipirila katundu wa order ngati afika ku shop Timamalizitsa kulipira ngati katundu tavomeleza kuti ndi emweyo... Ngati mli ndi mfunso inbox me.. Ndalama timabweza ngati munthu katundu omwe tamugulira ndiosephana... Muno sitigulitsa za copy... Only original... Tosaiwale kuti mukagula katundu transport ndilanu... Mwina ngati kulizositha zina ndimavomeleza kulipira ndikha.. ~ *Thank you all customer welcome..*