Search the WhatsAd Community Intelligence index of WhatsApp groups to find the best ones.
1 result in the WhatsAd group index
*TAKULANDIRANI KU TIPEZE WACHIKONDI 💓💓* *MALAMURO NDI AWA* 👇 *1️⃣ALIYENSE AKUYENERA KUTENGA NAWO MBALI KUTI MACHEZA AKOME KOMASO KUTI TIPEZE WACHIKONDI MOSAVUTA👩❤️💋👨👨❤️👨* *2️⃣MULENDO UKAFIKA AKUYENERA KUPONYA PIC NDI KUNENA KOMWE UMAKHALA💃🕺* 🤳 *3️⃣MA LINK AMA GROUP ENA MUNO AI 👺👺* 4️⃣ *MA PROGRAM ATHU ALI MOTERE:* *MONDAY, WEDNESDAY NDI FRIDAY TIMAKHALA NDI* *TOPIC. NDIPO SUNDAY NDI PIC DAY* 💃🕺🤳 *5️⃣NKHANI ZA KU INBOX ZIZITHERO KUMWEKO* 🫐🫐🫐🫐🫐 *6️⃣KUCHEZERANA KUZIWANA KUMAONONGA GROUP KUMACHEZA NDI ALIYENSE* 🤺 *7️⃣VOICE NOTE MUNO AI & WEEK ILIYONSE TIMACHOSA ANTHU OSATENGA NAWO MBALI* 🤺🏹 *🌹🌹🌹TIPEZE WACHIKONDI*
Verified invite link, member details and advertising options on WhatsAd.
𝕋𝕀ℙ𝔼ℤ𝔼 𝕄𝔸𝕃𝕀ℕ𝕂 𝕄𝕌ℕ𝕆 Welcome alendo nonse takulandilani khalani omasuka 🤸♀️🤸♀️🤸♀️🤸♀️🤸♀️🤸♀️🤸♀️🤸♀️🤸♀️muno timalola kuponya malink ndi macheza basi🤺🤺🤺🤺🤺🤺🤺🤺🤺🤺Zosaloledwa muno ndi izi👇🏻👇🏻 𝗭𝗮𝘀𝗶𝗻𝗴'𝗮𝗻𝗴𝗮 𝗭𝗮𝗺𝗮𝗹𝗼𝗻𝗱𝗮 𝗞𝘂𝗽𝗼𝗻𝘆𝗮 𝗹𝗶𝗻𝗸 𝘆𝗼𝗺𝘄𝗲 𝘆𝗼𝗺𝘄𝗲𝘆𝗼 𝗸𝗼𝗺𝗮 𝗺𝗼𝗯𝘄𝗲𝗿𝗲𝘇𝗮 𝗯𝘄𝗲𝗿𝗲𝘇𝗮 ✖️✖️✖️✖️✖️Anzathu onyozera ma 𝗿𝗲𝗺𝗼𝘃𝗲 🙏🏻🙏🏻🙏🏻🙏🏻🙏🏻
Sending movie
MALAMULO AGROUP INO NDI AWA✍️✍️👇👇👇 TIPEZE MALINK PANO 💯% 1 osatumiza ma video olaula kapena photo zolaura ukapezeka remove❌ 2 osatumiza zotsatsa malonda ukapezeka remove❌ 3 osatumiza ma stick ukapezeka remove❌ 4 Osatumiza zachipani ukapezeka remove❌ 5 Osatumiza ma vn kapena record ukapezeka remove❌ 6 tisasakhane mitundu ukapezeka remove❌ Kuponya malink ndi udindo wawina aliyese tiyeni tigawane ma link amene zathu wapepha zikomo Komaso kucheza ndikofunika Tiyeni ticheze Ma member nonse mukhare omasuka pamene mwalowa muno maramulo ndi amenewo tiyeni titsate malamuro kuti masiku okhara muno achuluke mwakoma nose munali ndine m'bale wanu mr Joseph admin anu baye ❤️🇲🇼🇲🇼
Welcome/Mwalandilidwa nonse♥️