Search the WhatsAd Community Intelligence index of WhatsApp groups to find the best ones.
1 result in the WhatsAd group index
Pano ndi pa group la dza mpila only malamulo agulu aliyense amadziwa cholinga chathu ndikuika ma sewelo ampila pa tsogolo ALiyese ali ndi ufulu oyangula pano
Verified invite link, member details and advertising options on WhatsAd.
Qr8aaw5e41a
Cholinga Cha group ndikukambirana nkhani zokhuza dela lathu lamakanjiri kundale zadela ,chitukuko komanso mavuto amdela MALAMULO A GROUP (1) osatumiza zithunzi kapena ma kanema olawula (2) osatumiza ma link ama group ena pamudzi pano (3) osatukwanizana pa group pano (4) kulemekeza maganizo anzathu ,sitingaganize mofanana (5) osatenga nkhani zokambidwa pano mwachisawawa chifukwa anthu akhala ndimaufula olankhula zakukhosi kwawo mosaopa (6) obwela ndichisokonezo sasowa ndipo sitizachedwa kum'panga remove (7) munthu Ali ndiufulu olemba kapena kugwiritsa ntchito mawu ake pogawana uthenga (8) osatumiza nkhani zabodza zopanda umboni pa group Kupezeka ophwanya malamulo adzachotsedwa pa group (9) Group la friends of makanjira liziyamikira kapena kudzudzula andale ,akapezeka munthu obweletsao chisokonezo pa group posafuna anthu kuti adzudzule kapena kuyamikira andale ,munthuyo adzachotsedwa pa group car h
Welcome to makanjira market place cholinga chathu ndikutha ndizana pa nkhani ya business tizitha kupeza katundu mosavuta aliyense ndiololedwa kugula kapena kugulitsa malonda. sitimalola kutukwanana kunyozana kuponya zolaula. potelo oswa lamulo azapezeka panja PA group NB kugula kapena kugulitsa katundu wakuba sitimalola ndipo akazakugwilani izo zizakhala vuto lanu aliyense ogula akuyenela kuonetsetsa kuti munthuyo katunduyo ndiwake komanso mboni izikhalapo