Search the WhatsAd Community Intelligence index of WhatsApp groups to find the best ones.
1 result in the WhatsAd group index
TAKURANDILANI KUCHIMAKE KWA NYIMBO MALAMULO ALI MOTERE 1.OSATUMIZA ZOLAWULA PA GROUP IRI KAPENA STICKER UKAPEZEKA REMOVE 2.MUNO MA VOICE RECORDING AKURETSEDWA ALIYESE AKUENERA KUREMBA 3.UKATUMIZA VIDEO OR AUDIO UKUYENERA KUREMBA TITLE YANYIMBOYO 4.KUTUKWANANIZANA MUNO AYI ALIYESE AZIREMBA DZINA LA NYIMBO YOMWE AKUFUNA 5.ZOSANKHANA MITUNDU MUNO AYI GYZ 6.KUREMBA TITLE ZIMATHANDIZA MUNTHU KUTI USATENGE NYIMBO YOTI ULINAYO KARE 7.UKAFUNA KUCHEDZA NDI MDZAKO KU INBOX UMUUZA AKALORA UPITA โ๏ธ๐ค๐ฅฐ 8.KU INBOX KO MUKAYAMBANA NKHAN IMENEYO OSABWERETSA PA GROUP MUKAPEZEKA ๐ชโโ ZIKOMO ANTHU NOSE MUGULUPU LIMENERI TIYENI TIPEZE NYIMBO ZA PAMTIMA PANTHU PANO ๐
Verified invite link, member details and advertising options on WhatsAd.
*NYIMBO ZOTAMANDA KOMANSO KUKWEZA YEHOVA*
We sell bed linen and blankets of different types from South Africa ๐ฟ๐ฆ. Admin amakhala kubalaka and South Africa
Malamulo a Muno ------------------------------ (1)Kupempha ndikutumiza nyimbo. (2)Nyimbo zake ziyambire 2010 kumatsika kumusi. (3)Osatukwanana wina ndimzake timalimbikitsa ubale muno. (4) Osatumiza link or ma Photo olaura kapenanso zosemphana ndi group lino muzachotsedwa. (5)Osanyozerana mtundu kapena chipembedzo tonse ndi amodzi. Komaso osaponya ma sticker muno ayi (6)Ndi udindo wa aliyense kutumiza ndikupempha nyimbo zakale koma ngati mwafuna zatsopano pemphani ku inbox ena azakupatsani komweko. (7) Ma voice note siololedwa muno koma zikavutitsitsa kuti mufuna nyimbo nde mutu wake simukuudziwa funsani admin aliyense kuti mumumvetseletse Voice note ndipo akusakireni . (8)Osatukwana muno tili ndi anthu akulu akulu azaka zapakanthawi omwe amafunika kuwalemekeza. Tiyeni titsate malamuro kuti tipitilize kusangalara ndinyimbo komanso zochitika zotikumbutsa kale lathu .
๐๐๐๐๐ MALAMULO ATHU ALI MOTERE ๐๐๐๐๐๐ 1 MVELANI MALAMULO A GROUP INO 2 KUCHEZA MOSASANKHANA MUTUNDU KOMASO KOCHOKERA POTI TOSE NDIFEANA ABANJA LIMODZI ๐ฅ๐ฅ๐ฅ๐ฅ๐ฅ๐ฅ๐ฅ๐ฅ๐ฅ๐ฅ๐ฅ๐ฅ๐ฅ 3 NDIUDINDO WA ALIYESE KUTUMIDZA MA VIDEOS AKUCHIPINDA KOMASO MAPIC MWAKATHITHI ๐๐ AMENE SAKUTENGA GAWO KWA 3 DAYS REMOVE ๐ฏ๐ฏ 4 MALINK AMAGULU ENA MUNO OSAPONYAMO CHONDE UKANGOPEZEKA OTERO REMOVE ๐บ๐บ๐บ๐บ๐บ๐บ๐บ๐บ 5 MA V N TISAGWILITSE NTCHITO KUOPAKUTI TINGAWATHERE BUNDLE ANTHU ENA COZ TIMAPEZA MO SIYANA NDALAMA YA BUNDLE NO STICKERS NO VOICE CHAT ๐๐๐๐๐๐๐๐๐๐๐ 6 TIZIKHALA NDI TOPIC LACHITATU LILILOSE NTHAWIYA 7 30 MAZULO๐ฟ๐ฟ๐ฟ๐ฟ๐ฟ๐ฟ๐ฟ๐ฟ๐๐๐๐๐๐๐ 7 SUNDY LILILOSE NDI PIC DAY ALIYESE AKUPEMPHEDWA KUPONYA PIC YAKE NDIKUFOTOKOZA NDI DZINA LAKE KOMASO KOMWEAKUKHALA ! KUPONYA PIC YAMWINIWAKE KULAKWA UKAPEZEKA REMOVEโ ๏ธโ ๏ธโ ๏ธ 8 MUKAFUNA KUFUSILANA PA GROUP POPANO KUPANGIRA ENA ALIPABANJA TINGAWATHESERE BANJA MUKAFUNA KULOWA KU IN BOX AUZENI PA GROUP POPANO KUTI NDIKHOZA KUFIKA KUSELIKO๐๐๐๐๐ MALAMULO ATHU ALI MOTERE ๐๐๐๐๐๐ 1 MVELANI MALAMULO A GROUP INO 2 KUCHEZA MOSASANKHANA MUTUNDU KOMASO KOCHOKERA POTI TOSE NDIFEANA ABANJA LIMODZI ๐ฅ๐ฅ๐ฅ๐ฅ๐ฅ๐ฅ๐ฅ๐ฅ๐ฅ๐ฅ๐ฅ๐ฅ๐ฅ 3 NDIUDINDO WA ALIYESE KUTUMIDZA MA VIDEOS AKUCHIPINDA KOMASO MAPIC MWAKATHITHI ๐๐ AMENE SAKUTENGA GAWO KWA 3 DAYS REMOVE ๐ฏ๐ฏ 4 MALINK AMAGULU ENA MUNO OSAPONYAMO CHONDE UKANGOPEZEKA OTERO REMOVE ๐บ๐บ๐บ๐บ๐บ๐บ๐บ๐บ 5 MA V N TISAGWILITSE NTCHITO KUOPAKUTI TINGAWATHERE BUNDLE ANTHU ENA COZ TIMAPEZA MO SIYANA NDALAMA YA BUNDLE NO STICKERS NO VOICE CHAT ๐๐๐๐๐๐๐๐๐๐๐ 6 TIZIKHALA NDI TOPIC LACHITATU LILILOSE NTHAWIYA 7 30 MAZULO๐ฟ๐ฟ๐ฟ๐ฟ๐ฟ๐ฟ๐ฟ๐ฟ๐๐๐๐๐๐๐ 7 SUNDY LILILOSE NDI PIC DAY ALIYESE AKUPEMPHEDWA KUPONYA PIC YAKE NDIKUFOTOKOZA NDI DZINA LAKE KOMASO KOMWEAKUKHALA ! KUPONYA PIC YAMWINIWAKE KULAKWA UKAPEZEKA REMOVEโ ๏ธโ ๏ธโ ๏ธ 8 MUKAFUNA KUFUSILANA PA GROUP POPANO KUPANGIRA ENA ALIPABANJA TINGAWATHESERE BANJA MUKAFUNA KULOWA KU IN BOX AUZENI PA GROUP POPANO KUTI NDIKHOZA KUFIKA KUSELIKO
*WELCOME TO KUGAWANA NYIMBO MWAKATHITHI*. ๐ซ๐ง๐ง๐ผ๐ต๐ต๐ถ *MALAMULO ATHU ALIMOTELE๐๐ผ๐๐ผ*. *1.๐ukangojoina kumene group yambakaye waponya pic... Yako ndikuzilongotsola dzina lako ndikomwe ukuchokera*. *2.๐Tilemekedzane wina ndinzache posatengera mtundu kapena chipembedzo or kochokera*.โโโ๐๐ซ *3.๐No ma videos kapena zithunzi zolawula muno even ma voice notesโโโ๐๐ซukangopedzeka remove๐ฌ๐ฎ*. *4.๐No any foreigner groups/links, ma short videos or stickers muno ayiโโโ๐๐ซukangotumidza basi uwona nsana wanjira๐ฌ๐ฎ*. *5.๐ndiudindo wawina aliyense otumidza nyimbo muno osamangodikira ma admin okha kuti atumidze nyimboโโโ๐๐ซ*. *6. ๐Then usanapemphe nyimbo yamba kaye waponya nyimbo zomwe iwe ulinazo ndipo ife tizakuthandidza the same time*. *7.๐Kupempha mowirikidza koma iwe osatumidza zimenezo ayinsoโโโ๐๐ซma camera akakuwona ๐basi remove ndiyomweyo๐ฌ๐ฎ*. *8.๐Ndipo osatenga nawo gawo pa maprograms amenewa timasazikana naye mosayang'ana nkhope๐คฃโโโ๐๐ฌ๐ฎ*. *โ ๏ธ๐ธWARNING: ngati wapedza kt group lakiyidwa๐๐๐๐osafunsa kt why?โโโ๐ Udzalandira remove ๐ฌ๐ฎndekuti ma admin akukonza zina zake zosemphana ndi group*. *#. โ โ Tsatilani zimenezi kt matsiku anu okhala muno achuluke musanawone nsana wanjira ngati omwe adawona John chilembwe kumandala๐*. *#. โ โ Machedza wez koma nyimbo kathithi...*. *WROTE BY ALL ADMINISTRATOR OFFICCERS, MWAKOMA NONSE๐ฅณ๐ฅณ๐๐ป๐๐ป๐คผโโ๏ธ๐คธ๐ปโโ๏ธ๐คธ๐ป๐๐ปโโ๏ธ๐๐๐ป๐๐ป*.
TAKULANDILANI KHALANI OMASUKA CHONDE TSATANI IZI KUTI. MUKHALITSE PAMALO PANO๐๐๐ 1. Link ya group Lina ayi๐ซ 2. Zolaula kuno ayi๐ซ 3. Zoyambana kutukwana ayi kunyozana ayi๐ซ 5. Ma voice recorder ayi ๐ซ 6. Ndiudindo waliyese kuponya filim TIPEZEN ADMIN KUTI TIKUTHANDIZENI ZAMAFILIM OMWE MUKUFUNA๐๐ 099130220 Mukafunaso VIP ILIPO MTENGO K2000 AKU JON OR MAYUNITS๐๐ฝ