Search the WhatsAd Community Intelligence index of WhatsApp groups to find the best ones.
1 result in the WhatsAd group index
๐๐โจ๏ธ
Verified invite link, member details and advertising options on WhatsAd.
*NYIMBO ZOTAMANDA KOMANSO KUKWEZA YEHOVA*
Malamulo a Muno ------------------------------ (1)Kupempha ndikutumiza nyimbo. (2)Nyimbo zake ziyambire 2010 kumatsika kumusi. (3)Osatukwanana wina ndimzake timalimbikitsa ubale muno. (4) Osatumiza link or ma Photo olaura kapenanso zosemphana ndi group lino muzachotsedwa. (5)Osanyozerana mtundu kapena chipembedzo tonse ndi amodzi. Komaso osaponya ma sticker muno ayi (6)Ndi udindo wa aliyense kutumiza ndikupempha nyimbo zakale koma ngati mwafuna zatsopano pemphani ku inbox ena azakupatsani komweko. (7) Ma voice note siololedwa muno koma zikavutitsitsa kuti mufuna nyimbo nde mutu wake simukuudziwa funsani admin aliyense kuti mumumvetseletse Voice note ndipo akusakireni . (8)Osatukwana muno tili ndi anthu akulu akulu azaka zapakanthawi omwe amafunika kuwalemekeza. Tiyeni titsate malamuro kuti tipitilize kusangalara ndinyimbo komanso zochitika zotikumbutsa kale lathu .
๐ณ๐ณ๐ณ๐ณ Takulandilani kuno ku group la โ๏ธโ๏ธ KUCHIMAKE KWA MA LINKS ๐ช ๐ช ๐ซ๐ซ๐ฉโโค๏ธโ๐โ๐ฉ๐ด๐ด๐ด๐ด๐ด ๐๐๐๐๐๐๐๐๐๐ ๐ซง๐ซง Malamulo anthu ali motere๐ฆ๐ฆ๐ง๐๐๐ ๐๐๐๐๐๐๐๐๐ 1๐ณ๐ณโ๏ธ Ngati mwalowa kumene mu group lino mukupemphedwa kuponya ๐ธ Pic ๐ธyanu ๐๐ฝโโ๏ธ dzina lanu๐๐ฝโโ๏ธkomaso komwe mumakhala๐๏ธkuti tikudziweniโ๏ธโ๏ธ 2๐ณ๐ณโ๏ธndi udindo wa aliyese kuponya ma link โ๏ธโ๏ธ 3๐ณ๐ณโ๏ธAno simalo opangila business kapena ndale โโ 4๐ณ๐ณmacheza ndi oloredwaโโ 4๐ณ๐ณโ๏ธOsaponya ma video ngakhaleso ma pic olaulaโโ 5๐ณ๐ณโ๏ธMa sticker siololedwaโโ 6๐ณ๐ณโ๏ธMa VN ayiโโ 7๐ณ๐ณโ๏ธ Zilankhulo zololedwa muno ndi English komanso Chichewa 8๐ณ๐ณโ๏ธ Ngati mwayambana kwinako zisafike muno โโ 9๐ณ๐ณโ๏ธ Ngati mwakondana Tengelanani ku imbox ๐๐ 10๐ณ๐ณโ๏ธOsalowa ku imbox kwa munthu popanda chilolezoโ๏ธ 11๐ณ๐ณโ๏ธ Sunday iriyonse timakhala ndi ๐ธ PIC DAY๐ธkuyambila nthawi ya 08:00hrsโmpakana kufikila nthawi ya 21:00hrsโโ๏ธ ๐ชผ๐ชผ๐ชผ๐ชผ๐ชผ๐ชผ๐ชผ๐ชผ๐ชผ๐ชผ๐ชผ๐ชผ๐ชผ๐ชผ๐ชผ๐ชผ๐ชผ๐ชผ๐ชผ๐ชผ ๐ฆ๐ฆMwakoma nonse nkhalani omasuka๐๐๐๐๐๐๐๐๐๐๐๐๐๐๐๐๐๐๐๐๐๐๐
[contact hidden]